Growing Money Minds

Call Directions Contact the business

Growing Money Minds Money Coach | Malawi. Helping you stop being broke with simple money habits that work.

‼️WhatsApp yathu tiyeni tiyiteteze potsatira njira izi.‼️Kuwonjezera apa, pewani kumangopanga click/kudina ma link ku Wh...
20/10/2026

‼️WhatsApp yathu tiyeni tiyiteteze potsatira njira izi.‼️

Kuwonjezera apa, pewani kumangopanga click/kudina ma link ku WhatsApp nwachisawawa. Olo atakhala ndi munthu omudziwa.

Samalani.

TETEZANI AKAUNTI YANU YA WHATSAPP

Tsegulani ndi kutsimikizira kawiri kuti muonjezere chitetezo

Mmene mungatetezere tsamba lanu la mchezo (WhatsApp) :
1. Pitani kumadongosolo (settings)
2. Dinani pa akaunti (Account)
3. Tsakhani "kutsimikizira kawiri" (Two step verification)
4. Tsatirani malangizo kuti mumalidzitse

Khalani otetezeka pa matsamba a mchezo!




20/10/2026

Tisabalalike ayi!
Inu mukuona bwanji?

20/10/2026

Kuthandiza achibale ndi kwabwino, koma thandizani mogwirizana ndi ndalama zomwe muli nazo.
Good morning!

Poverty is not just a lack of money; it is a relentless cycle that traps generations. But what if the key to breaking th...
19/10/2026

Poverty is not just a lack of money; it is a relentless cycle that traps generations.
But what if the key to breaking that cycle is not a miracle, but a habit?
Today, we look at the mechanics of poverty and how simple financial disciplines act as the hammer that shatters the glass ceiling of generational poverty. 💥

17/10/2026

Unit Trust Series part 1.

Tiyeni tiwonere iyi ndi ma part ena onse 5 ofotokozera za ma Unit Trust.

16/10/2026

Mugule ma Shares kapena ma Unit Trust?

For paid consultations, WhatsApp 0882 765 990.

Pliny the Elder said this 2,000 years ago, and it still rings true. We plan for the best, but we must prepare for the wo...
16/10/2026

Pliny the Elder said this 2,000 years ago, and it still rings true. We plan for the best, but we must prepare for the worst.
Life is unpredictable. Markets fluctuate, health fails, and accidents happen.
The question is not if something will happen, but when, and will you be ready?

Risk management is not about being pessimistic; it's about being a realist.
We buy insurance not because we expect to crash the car, but because we know we are human. We invest in insurance because we love our families and want to ensure they are taken care of, no matter what the future holds. Accepting uncertainty is the first step to being prepared for it.

Preparation is the antidote to anxiety. When you have a risk management plan in place, you can stop worrying about the "what ifs" and start living in the present.

💐❤️ HAPPY MOTHER’S DAY, MAMAS!❤️ 🇲🇼Lero, tikusangalalila azimayi okongola inu omwe mumakonda, mumadzipeleka, mumasamala ...
15/10/2026

💐❤️ HAPPY MOTHER’S DAY, MAMAS!❤️ 🇲🇼

Lero, tikusangalalila azimayi okongola inu omwe mumakonda, mumadzipeleka, mumasamala ndi kugwira ntchito mosatopa kuti mabanja anu akhale ndi moyo wabwino.

Kuchokera kwa mayi yemwe akupanga business yaying'ono, kapena ndi mlimi kumudzi, ogwira ntchito mu ofesi, mayi yemwe anasankha kusamala ana kunyumba ndi mayi wayekha yemwe akuyesetsa kuti zinthu ziyendebe; timakuonani, timakunyadilani ndipo ndinu ofunikila kwambiri! 🫶🏽

Ine ngati mayi, kulandira card iyi kwa mwana wanga lero, kwandikumbutsa kuti pena, mphatso zikuluzikulu sizifuna ndalama zambiri. Ndi chikondi, malingaliro abwino, ndi nthawi yabwino yomwe timakhala nayo ndi ana athu.

Kwa mayi aliyense akuwerenga izi; tikukufunirani kupeza mphamvu pomwe mwatopa, chisangalalo mu zinthu zing'onozing'ono komanso mzeru kuti mukhonze tsogolo labwino la inu ndi banja lanu.

Happy Mother’s Day from US! 💜💛🧡

The hustle is real, but so are the risks. Whether you are a salaried employee or a busy entrepreneur, you have people re...
14/10/2026

The hustle is real, but so are the risks. Whether you are a salaried employee or a busy entrepreneur, you have people relying on your income. Are you protecting that income?
Here are the four pillars of risk management you should not ignore.

14/10/2026

Kupeza ndalama zowonjezela pa zimene umapeza sikutanthauza kuti udzakhala wolemera.
Good Morning 🌄

Address

Lilongwe

Opening Hours

Monday 06:00 - 18:00
Tuesday 06:00 - 18:00
Wednesday 06:00 - 18:00
Thursday 06:00 - 18:00
Friday 06:00 - 18:00
Saturday 08:00 - 17:00
Sunday 13:00 - 18:00

Telephone

0882765990

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Growing Money Minds posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Growing Money Minds:

Shortcuts

Share

Category