FunMan Aseh

FunMan Aseh Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from FunMan Aseh, Financial service, Kanengo, Lilongwe.

22/10/2024

Triephornia Thomson Mpinganjira

Ayi zikomo kukupemphani ya promote FDH Bank Anthem osatipanga respond okay mulungu akudalitseni ndithu πŸ‘

Okondedwa madam Triephornia Thomson Mpinganjira πŸ™Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la Facebook ko...
17/10/2024

Okondedwa madam Triephornia Thomson Mpinganjira πŸ™

Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la Facebook koma chifukwa chakuvuta kulumikizana Nanu bolani munvetsetse uthengawu πŸ‘

Munthune ndinaimba nyimbo yanga yoyamikira ntchito za FDH Bank Plc - Malawi kuti mwina amene sananveko za Bank Yi kapena ubwino wake adziwe ndipo mwa a Malawi ena omwe nyimboyo inakwanitsa kunvera nyimboyo anailandira ndipo anakatsekula ma account a FDH Bank asakufuna chifukwa cha uthengawu πŸ‘‹

Ndinayesetsa kupempha thandizo loti nyimboyo ifikire dziko lonse la Malawi komaso ikhale ndi video πŸ“Έ yake yake koma zidakanika chifukwa anthu akewo samandithandiza amangoti uthengawu upite Kaye kulikulu kwa inuyo mabwana a FDH Bank

Ndiye Relo patatha zaka zitatu ndatibe nsangozisiya ayi koma ndikupempheni kuti munvele Kaye nyimboyo ndipo ngati ingakusangalatseni muyese kundithandiza kuti nyimboyo ifikire ku mtundu wa amalawi ndipo ikhale ndi video chifukwa kwathu kuno anthu anaitcha FDH ANTHEM chifukwanso Ili ngati advert mwapadera πŸ™ pandekha mnayesetsa kuiyika pa internet kuti ena iwafikire zikomo madam chonde ndithandizeni mulimosemo kuti ndipushire nyimboyo πŸ™

FunMan FDH Bank πŸ‘‰πŸ‘‰πŸ‘‰

Check out FDH Bank (Prod. Mimeshak) by Fun Man. This 03:32 Afrobeat from Malawi's #1 source of entertainment malawi-music.com.

Osauka satopa 🌍Okondedwa madam Triephornia Thomson Mpinganjira πŸ™Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba...
14/10/2024

Osauka satopa 🌍

Okondedwa madam Triephornia Thomson Mpinganjira πŸ™

Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la Facebook koma chifukwa chakuvuta kulumikizana Nanu bolani munvetsetse uthengawu πŸ‘

Munthune ndinaimba nyimbo yanga yoyamikira ntchito za FDH Bank Plc - Malawi kuti mwina amene sananveko za Bank Yi kapena ubwino wake adziwe ndipo mwa a Malawi ena omwe nyimboyo inakwanitsa kunvera nyimboyo anailandira ndipo anakatsekula ma account a FDH Bank asakufuna chifukwa cha uthengawu πŸ‘‹

Ndinayesetsa kupempha thandizo loti nyimboyo ifikire dziko lonse la Malawi komaso ikhale ndi video πŸ“Έ yake yake koma zidakanika chifukwa anthu akewo samandithandiza amangoti uthengawu upite Kaye kulikulu kwa inuyo mabwana a FDH Bank

Ndiye Relo patatha zaka zitatu ndatibe nsangozisiya ayi koma ndikupempheni kuti munvele Kaye nyimboyo ndipo ngati ingakusangalatseni muyese kundithandiza kuti nyimboyo ifikire ku mtundu wa amalawi ndipo ikhale ndi video chifukwa kwathu kuno anthu anaitcha FDH ANTHEM chifukwanso Ili ngati advert mwapadera πŸ™ pandekha mnayesetsa kuiyika pa internet kuti ena iwafikire zikomo madam chonde ndithandizeni mulimosemo kuti ndipushire nyimboyo πŸ™

FunMan FDH Bank πŸ‘‰πŸ‘‰πŸ‘‰

Check out FDH Bank (Prod. Mimeshak) by Fun Man. This 03:32 Afrobeat from Malawi's #1 source of entertainment malawi-music.com.

Okondedwa madam Triephornia Thomson Mpinganjira  πŸ™Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la Facebook k...
10/10/2024

Okondedwa madam Triephornia Triephornia Thomson Mpinganjira πŸ™Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la...
10/10/2024

Okondedwa madam Triephornia Triephornia Thomson Mpinganjira πŸ™

Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la Facebook koma chifukwa chakuvuta kulumikizana Nanu bolani munvetsetse uthengawu πŸ‘

Munthune ndinaimba nyimbo yanga yoyamikira ntchito za FDH Bank Plc - Malawi kuti mwina amene sananveko za Bank Yi kapena ubwino wake adziwe ndipo mwa a Malawi ena omwe nyimboyo inakwanitsa kunvera nyimboyo anailandira ndipo anakatsekula ma account a FDH Bank asakufuna chifukwa cha uthengawu πŸ‘‹

Ndinayesetsa kupempha thandizo loti nyimboyo ifikire dziko lonse la Malawi komaso ikhale ndi video πŸ“Έ yake yake koma zidakanika chifukwa anthu akewo samandithandiza amangoti uthengawu upite Kaye kulikulu kwa inuyo mabwana a FDH Bank

Ndiye Relo patatha zaka zitatu ndatibe nsangozisiya ayi koma ndikupempheni kuti munvele Kaye nyimboyo ndipo ngati ingakusangalatseni muyese kundithandiza kuti nyimboyo ifikire ku mtundu wa amalawi ndipo ikhale ndi video chifukwa kwathu kuno anthu anaitcha FDH ANTHEM chifukwanso Ili ngati advert mwapadera πŸ™ pandekha mnayesetsa kuiyika pa internet kuti ena iwafikire zikomo madam chonde ndithandizeni mulimosemo kuti ndipushire nyimboyo πŸ™

FunMan FDH Bank πŸ‘‰πŸ‘‰πŸ‘‰https://www.malawi-music.com/F/3559-fun-man/10423-fdh-bank/16361-fdh-bank-prod-mimeshak

Okondedwa madam Triephornia Thomson Mpinganjira  πŸ™Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la Facebook k...
10/10/2024

Okondedwa madam Triephornia Thomson Mpinganjira πŸ™

Choyamba ndipepese chifukwa ndalemba uthengawu pa tsamba la Facebook koma chifukwa chakuvuta kulumikizana Nanu bolani munvetsetse uthengawu πŸ‘

Munthune ndinaimba nyimbo yanga yoyamikira ntchito za FDH Bank Plc - Malawi kuti mwina amene sananveko za Bank Yi kapena ubwino wake adziwe ndipo mwa a Malawi ena omwe nyimboyo inakwanitsa kunvera nyimboyo anailandira ndipo anakatsekula ma account a FDH Bank asakufuna chifukwa cha uthengawu πŸ‘‹

Ndinayesetsa kupempha thandizo loti nyimboyo ifikire dziko lonse la Malawi komaso ikhale ndi video πŸ“Έ yake yake koma zidakanika chifukwa anthu akewo samandithandiza amangoti uthengawu upite Kaye kulikulu kwa inuyo mabwana a FDH Bank

Ndiye Relo patatha zaka zitatu ndatibe nsangozisiya ayi koma ndikupempheni kuti munvele Kaye nyimboyo ndipo ngati ingakusangalatseni muyese kundithandiza kuti nyimboyo ifikire ku mtundu wa amalawi ndipo ikhale ndi video chifukwa kwathu kuno anthu anaitcha FDH ANTHEM chifukwanso Ili ngati advert mwapadera πŸ™ pandekha mnayesetsa kuiyika pa internet kuti ena iwafikire zikomo madam chonde ndithandizeni mulimosemo kuti ndipushire nyimboyo πŸ™

FunMan FDH Bank πŸ‘‰πŸ‘‰πŸ‘‰https://www.malawi-music.com/F/3559-fun-man/10423-fdh-bank/16361-fdh-bank-prod-mimeshak

05/10/2024

Ndiochepa amene amakondwa mukamapambana 😚
Pray for them πŸ™

08/09/2023

08 September 2023

Dr Namadingo

Address

Kanengo
Lilongwe
265

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when FunMan Aseh posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share