Go Jet Investments

Go Jet Investments We sell farm inputs such as Agri chemicals,fertilizer and farm tools, we also buy farm produce like soya beans,groundnuts and maize

30/05/2026

Don't wait for October to start looking for inputs. Secure your fertilizer and seed now through small weekly deposits.

๐Ÿ”ฅ TETEZANI CHIMANGA CHANU NDI WIVOKIL SUPER 275 EC! ๐Ÿ”ฅ (WA MADZI)Musalole tizilombo kuwononga chimanga chanu mukachisunga...
29/05/2026

๐Ÿ”ฅ TETEZANI CHIMANGA CHANU NDI WIVOKIL SUPER 275 EC! ๐Ÿ”ฅ (WA MADZI)

Musalole tizilombo kuwononga chimanga chanu mukachisunga.
WIVOKIL SUPER 275 EC Grain Protectant ndi mankhwala odalirika oteteza chimanga ku tizirombo ta mโ€™nyumba yosungiramo.

๐ŸŒฝ Botolo limodzi limagwira ntchito pa matumba 200 a chimanga cha 50kg
๐Ÿ’ฐ Mtengo wake ndi MK100,000 yokha
๐Ÿ“ Zikupezeka ku GO-JET Investments ku Olympic Mall

โœ… Amateteza bwino ku tizirombo ta mโ€™chimanga
โœ… Amathandiza kuchepetsa kutayika kwa zokolola
โœ… Osavuta kugwiritsa ntchito
โœ… Oyenera alimi, amalonda ndi osunga chimanga

Musataye zokolola zanu mutavutika kulima.
Gulani WIVOKIL SUPER 275 EC Wa MADZI lero ku GO-JET Investments!

๐Ÿ“ž Kuti mudziwe zambiri imbani:
+265 881 12 33 83

27/05/2026

Partner wathu Go Jet Investments has entered into an agreement with Horizon kuti adzithandizira distribution ya OSHO products!

Ndekuti now you can find ma products awawa kwa Partner wathuyu!

Check out at your nearest GoJet Shop!

One Africa Celebrating our heritage, Building Africa's future
25/05/2026

One Africa Celebrating our heritage, Building Africa's future

25/05/2026

We are grateful for communities that welcomed us and customers that turned into family. Have a great week.

22/05/2026

Tatsanzikana nawo alendo athu; it has been a wonderful experience meeting them and learning from them!

As they fly back to Lilongwe, we pray for Godโ€™s blessings upon them. The tickets were bought by Royal Travels and Village Market Home

Ku Lilongwe Partner Maziko Cars & General Dealers akawalandira and take them ku Lolos fashion plug ku Area 18B where madam Chunga will get herself a dress.

Kenako Maziko will take them to Nkhotakota.

Partner Go Jet Investments, ndalama munatipatsa ija yoti akafikirepo together with ya Anonymous K300,000 tawapatsa.

May God bless everyone who has made this a success๐Ÿ™โค๏ธ

Working closely with ๐—ž๐—ฎ๐˜€๐˜‚๐—ป๐—ด๐˜‚ ๐——๐—ถ๐˜€๐˜๐—ฟ๐—ถ๐—ฐ๐˜ ๐—”๐—ด๐—ฟ๐—ถ๐—ฐ๐˜‚๐—น๐˜๐˜‚๐—ฟ๐—ฎ๐—น ๐—ง๐—ฒ๐—ฐ๐—ต๐—ป๐—ถ๐—ฐ๐—ฎ๐—น ๐—ฎ๐—ฟ๐—บ๐˜€ and interacting with farmers in the ๐— ๐—ฎ๐—น๐—ฒ๐—บ๐—ถ๐—ฎ ๐—ฎ๐—ฟ๐—ฒ๐—ฎ, we c...
22/05/2026

Working closely with ๐—ž๐—ฎ๐˜€๐˜‚๐—ป๐—ด๐˜‚ ๐——๐—ถ๐˜€๐˜๐—ฟ๐—ถ๐—ฐ๐˜ ๐—”๐—ด๐—ฟ๐—ถ๐—ฐ๐˜‚๐—น๐˜๐˜‚๐—ฟ๐—ฎ๐—น ๐—ง๐—ฒ๐—ฐ๐—ต๐—ป๐—ถ๐—ฐ๐—ฎ๐—น ๐—ฎ๐—ฟ๐—บ๐˜€ and interacting with farmers in the ๐— ๐—ฎ๐—น๐—ฒ๐—บ๐—ถ๐—ฎ ๐—ฎ๐—ฟ๐—ฒ๐—ฎ, we continue learning where we can improve and strengthen our service delivery. Encouragingly, farmers are ready and eager to work with Gojet Investments as we build sustainable agricultural partnerships together.

20/05/2026

Admin ndi wa Arsenal akuti timpatse holiday ya 2 months. Mulola

Timakhala ndi makhwala osiyanasiyana opha tiziliombo tosiyanasiyana topezeka Kumunda komanso mnyumba.Mukumuonayi ndi Ter...
20/05/2026

Timakhala ndi makhwala osiyanasiyana opha tiziliombo tosiyanasiyana topezeka Kumunda komanso mnyumba.

Mukumuonayi ndi Termisnow omwe ndi mankhwala achiswe Mnyumba.

Kuti mudziwe zambiri imbani +265 997 834 102

Kumbukirani, Lachitatu lirironse timakhala ndi Pologalamu yathu ya Sikadzakokha pa wayilesi ya Zodiak. Nthawi ndi 4:30 m...
20/05/2026

Kumbukirani, Lachitatu lirironse timakhala ndi Pologalamu yathu ya Sikadzakokha pa wayilesi ya Zodiak. Nthawi ndi 4:30 masana.

Address

Private Bag B411
Lilongwe

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00
Friday 09:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 17:00

Telephone

+265888619772

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Go Jet Investments posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Go Jet Investments:

Share