ZWIDE

ZWIDE Real life talk | Money & daily struggles 🇲🇼
Best investment Relatable content every day Follow for more
(1)

07/08/2026
07/08/2026

Lero pa 7 August ndi tsiku lomwe ma share omwe anagulidwa aja akuikidwa mu account ya ma investors
Account ija amaitchula kuti Central Securities Depository (CSD Account)

Izi zikutanthauza kuti ma share wa atha kuonekano mu account yanu kuyambira lero koma sizingatheke kuti muwagulitse kapena kuti wina akuguleni

Koma mtati musuzumire mu account mwanu m***a kuwaona

Kuyambira Monday likudzali pa 10 August 2026
Ma share wa akhala aonekano pa Mainboard ya MSE

Izitu zikutanthauza kuti anthu atha kuyamba kugulaso kapena kugulitsa ma share a CHL plc



CHL munaiona kumenekoTesting Testing Loading 79%
07/08/2026

CHL munaiona kumeneko
Testing Testing
Loading 79%

07/08/2026

A very Good morning ILLOVO, BHL and MPICO shareholders
Tikuti mwadzuka bwanji inuyo?

Masiku nkumathamangira ku 10 August Red red red
06/08/2026

Masiku nkumathamangira ku 10 August

Red red red

Nthawi zina zimatha kumaoneka ngati ukupanga loss komatu ai Ukaigwiritsa bwino nthawi ntchito umangonva amzakonakudandau...
06/08/2026

Nthawi zina zimatha kumaoneka ngati ukupanga loss komatu ai
Ukaigwiritsa bwino nthawi ntchito umangonva amzakonakudandaula iwe ukupanga nawoso zomwezo nkumadabwa kuti awa akudandaula chani

Enatu share yomwe ya NBS yi anaigula pa MK149 sikaleso ai akamaiona inafika ku K1000 pano ili pa 600 nkanthu alibe nkhawa ai chifukwa iwo ngakhale zikuoneka ngati apanga loss komabe apanga qualify mu quoter final

Congratulations ma Scoarchers inuyo nthawi munaigwiritsa bwino ntchito ngati shareholder otsogola wa NICO emwe anaigula share ili pa K200 anthu akuopa kuti yakwera kwambiri lero ili pa K1 300 ena akuopaso ati itha kutsika kwambiri

Inu munachita machawi kupha make chulu Nigeria yomwe anthu amaiopa kwambiri ngakhale neba wakuswani koma ai ndithu zanu zili pa bwino

Congratulations ma shareholders omwe ngakhale ma share price akutsika koma inu muli pa easy kugulabe ndipo capital yanu ili intact

MK42 billion ndi ndalama zomwe zaperekedwa kwa ma shareholders kuchokera ku Company ya NICO ndalamazi zachokera kuphindu...
05/08/2026

MK42 billion ndi ndalama zomwe zaperekedwa kwa ma shareholders kuchokera ku Company ya NICO ndalamazi zachokera kuphindu limene company yapanga mu chaka cha chawo cha business cha 2025

Ndalamazi zagawidwa kwa ma shareholders kokwanila ka nayi

Ma dividends ndi lina mwa phindu lomwe anthu omwe amakhala ndi umwini ma company amapeza

Tikutitu MK42 billion


I can confirm msika ukuyenda bwino Ndipo am very happy kwambiri
05/08/2026

I can confirm msika ukuyenda bwino

Ndipo am very happy kwambiri

05/08/2026

NBS ndi Sunbird Shareholders
Ofcourse ma shareholders a NBS ululu anapima nawo
Koma Ku Sunbird uko

Opetuza mwati iyi itha bwanji?
05/08/2026

Opetuza mwati iyi itha bwanji?

Address

Blantyre

Telephone

+265998838518

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when ZWIDE posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to ZWIDE:

Share