Credit Data CRB

Credit Data CRB Credit Data CRB Ltd is a licensed credit reference bureau operating in Malawi
Phone: 0211831388 / 887618930
We are in Umoyo House Ground Floor, Blantyre

UWU NDI UTHENGA OFUNIKIRA WA NDONDOMEKO YOKHUZA MADANDAULO A LIPOTI LANUChonde werengani mwachidwi.❗ Akasitomala choyamb...
27/05/2026

UWU NDI UTHENGA OFUNIKIRA WA NDONDOMEKO YOKHUZA MADANDAULO A LIPOTI LANU

Chonde werengani mwachidwi.❗

Akasitomala choyamba dziwani kuti ndi ufulu wanu kutsutsa mbiri yomwe ife tikusungira ya inu ngati ili yosiyana ndi m’mene zikuyenera kukhalila. Mungathe kutelo pofila fomu yadandaulo kwa ife kapena ku bank ndi mabungwe obweleketsa ndalama kuti tikukonzeleni.
Chofunika kudziwa ndichakuti, mukakanidwa kutenga ngongole ku bank kapena mabungwe obwelekesa ndalama pazifukwa zoti munalephera kubweza ngongole kapena mavuto ena ndi bungwe lina zimayenela kuti mukonzetse lipoti lanu.

Dandaulo lanu likatipedza, timayenela kuwunikila bwino kuti tidziwe pomwe pali vuto. Kotelo nthawi zina zimatha kutheka kuti vutolo tingathe kulikonza tokha konkuno ndipo nthawi zina zimatengela kuti bungwe limene munatengako ngongole kapena lomwe lawoneka pa lipoti kuti muli nalo ngongole lititumizire ife mbiri (information) yanu yoyenera, kotelo ife a Credit Data timakhala tikudikila iwo kuti atelo kuti zitheke.

Dziwani kuti ndondomeko yokonza dandaulo lanu timagwila limodzi ndi mabungwe ena ndipo ife sitichosa vuto pa lipoti lanu opanda mabungwe omwe mwawatchulawo kutipatsa mbiri (information) yoyenela. Kukonza dandaulo kumatenga masiku khumi ogwila ntchito (10 working Days). Nthawi Zina pomwe masiku apitilira khumi, zimakhala kuti bungwelo lachedwa kutipatsa ife information yanu kuti tikukonzeleni.

Musanafunsire ngongole kulikonse yambani mwadziwa kaye zomwe zilipa lipoti lanu kuti musakanidwe ngongole.
Kudziwa mbiri yanu ya ngongole mwachangu kumakuthandidzilaninso kukonzeratu zolakwika pa lipotilo.

Mukafuna kudziwa zambili, tiyimbileni pa: 099 66 88 134 kapena tipezeni pa WhatsApp: 0887 61 89 30 or 098 55 36 528 || Tikupezeka mu Umoyo House Ground Floor, Ku Blantyre | www.creditdatamw.com

Akasitomala dziwani kuti, Inu ngati nzika ya Malawi ndi ufulu wanu kuona lipoti lanu la ngongole mwa ulere kamodzi pacha...
26/05/2026

Akasitomala dziwani kuti, Inu ngati nzika ya Malawi ndi ufulu wanu kuona lipoti lanu la ngongole mwa ulere kamodzi pachaka ku office yathu.

Koma ngati mulikutali mungathe kupeza lipoti lanu kudzela m’njira izi; pa WhatsApp, kapena Email, pa mtengo wa K5,000 yokha basi.
Musanafunsile ngongole kulikonse yambani mwadziwa kaye zomwe zilipa lipoti lanu kuti musakanidwe ngongole.
Kudziwa mbiri yanu ya ngongole mwachangu kumakuthandizilaninso kukonzelatu zolakwika pa lipotilo.

Mukafuna kudziwa zambili, tiyimbileni pa: 099 66 88 134 kapena tipezeni pa WhatsApp: 0887 61 89 30 or 0985536528 || Tikupezeka mu Umoyo House Ground Floor, Blantyre | www.creditdatamw.com

Africa is not just a place; it’s a heartbeat, a story, a union and a future. BE THE FIRST TO KNOW
25/05/2026

Africa is not just a place; it’s a heartbeat, a story, a union and a future.

BE THE FIRST TO KNOW



Celebrating the beauty, strength, and greatness of Africa today and always.Africa is not just a place; it’s a heartbeat,...
25/05/2026

Celebrating the beauty, strength, and greatness of Africa today and always.

Africa is not just a place; it’s a heartbeat, a story, and a future.



Osadikira mpaka ngongole Yanu ikanikeYambani mwawona credit report yanu lero.We are here to help you.Imbani kapena tilem...
22/05/2026

Osadikira mpaka ngongole Yanu ikanike
Yambani mwawona credit report yanu lero.

We are here to help you.

Imbani kapena tilembeleni message pa 0887618930


14/05/2026
Today, We join the public in Honoring the Father and Founder of Our Nation.Happy Kamuzu Day
14/05/2026

Today, We join the public in Honoring the Father and Founder of Our Nation.

Happy Kamuzu Day


WE ARE HIRING 📌 -A Systems Administrations OfficerAn opportunity to join our team. More details in the picture below.www...
08/05/2026

WE ARE HIRING 📌

-A Systems Administrations Officer

An opportunity to join our team.
More details in the picture below.

www.creditdatamw.com

Mu mwezi wa April wathawu, tinalandira madandaulo 1,583 ndipo tinatha kuthana ndi 1,528 mwa iwo.Tiliodzipereka kuthandiz...
06/05/2026

Mu mwezi wa April wathawu, tinalandira madandaulo 1,583 ndipo tinatha kuthana ndi 1,528 mwa iwo.

Tiliodzipereka kuthandiza makasitomala athu, chifukwa timadziwa kufunika kokhala ndi mbili yolondola yokhuza zangongole.
Ngati mwaona cholakwika chilichonse, musazengereze kulumikizana nafe. Tili pano kukuthandizani kuti muthe kukatenga ngongole kulikonse mosavuta.

Mukafuna kudziwa zambili, tiyimbileni pa 099 66 88 134 kapena 0887 61 89 30 |Tikupezeka mu Umoyo House Ground Floor, Blantyre | www.creditdatamw.com

Lachisanu lapitali Pa 1 May tinaliku CI Parish komwe kunali msonkhano wa Catholic Men's Association ndipo Anthu ambili a...
04/05/2026

Lachisanu lapitali Pa 1 May tinaliku CI Parish komwe kunali msonkhano wa Catholic Men's Association ndipo Anthu ambili anali ndikuthekela kowona, ndikudziwa Lipoti lawo lazangongole mwaulele.

‎Ena atawona kufunikila kwalipotili anagula kuti akhale nalo. Nanuso m***a kutipeza mwayi owona Lipoti lanu lero.

‎Tidziwiseni ngati mulindi zochitika m'dela lanu tizabwela kuzaika tebulo yathu kuti Inu muzathe kuwona ndikugula Lipoti lanu.


CELEBRATING LABOUR DAY!‎Every day you work hard to build your future — make sure your credit story reflects it. This Lab...
01/05/2026

CELEBRATING LABOUR DAY!

Every day you work hard to build your future — make sure your credit story reflects it. This Labour Day, we celebrate YOU.


‎ …

Address

Umoyo House Ground Floor, Victoria Avenue
Blantyre
P.O.BOX32153,CHICHIRI,BLANTYRE3

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00

Telephone

+265211831388

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Credit Data CRB posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Credit Data CRB:

Share