27/05/2026
ZITSAMBA GROUP LOANS
Ngongole zammagulu ammisika
ZOFUNIKIRA:
1. Chaunzika kwa mamembala onse
2. Mapu ojambula a malo okhala a anthu onse
3. Gwero la ndalama za mamembala
4. Mgwirizano wa mamembala
5. Kuvomerezeka kwa gulu
6. Kudzipereka pagulu kubweza
7. Gulu lamamembala atatu mpaka asanu
Imbani foni pama nambala awa;
0 111 828 108/109 or 0888111725 (Calls and Whatsapp) kapena tumizani email ku [email protected] kapena SMS