T.G. Dynamic Investments in All Poultry Businesses - Malawi

T.G. Dynamic Investments in All Poultry Businesses - Malawi TG DYNAMIC INVESTMENTS IN ALL POULTRY BUSINESSES, is a page that will only focus on Agribusiness but mainly on Poultry products and services.

Currently, we have opened a Broiler Chicken House, buy us

*Magik Powder*🚨Msati mchedwe nkumadikilira kuti ziyambe kudwala kupanga Chitosi Cha (chobiliwira) Green. *CHITOPA*  chim...
20/03/2024

*Magik Powder*
🚨Msati mchedwe nkumadikilira kuti ziyambe kudwala kupanga Chitosi Cha (chobiliwira) Green. *CHITOPA* chimatha kusesa khola lonse alimi anzanga.

*NDONDOMEKO YABWINO*
1. Perekani Katemera.
2. Use *Magik Powder* & boost the immunity to keep diseases at bay. Surely, *Magik Powder* will change the narrative & set you on a course to expand your poultry farm.

*KOMANSO NGATI👇*
🤏Zikuonetsa Chitosi Cha magazi. Pewani poonetsetsa kuti mukhola ndi mouma nthawi zonse.

*MAGIK POWDER* amathandizanso👇
✍🏼Kutupa kwa maso ndi mutu, Chifuwa, Kugwa mapiko, Chinfine, Kusowa chilakolako chokudya(APPETITE). Ndi mavuto/matenda ena.

*🌱MK8,000* 250grams

🇲🇼M-vet
*Even Chicks recommend us*to

*Magik Powder KU BLANTYRE.*▪️Awa ndi mankhwala a *organic* (herbs) a mbalame monga nkhuku, zinziri, abakha, nkhunda, nkh...
21/08/2022

*Magik Powder KU BLANTYRE.*
▪️Awa ndi mankhwala a *organic* (herbs) a mbalame monga nkhuku, zinziri, abakha, nkhunda, nkhanga ndi nkhukundembo.
▪️Mankhwalawa amathandiza ku matenda awa
🌾Chitosi cha magazi
🌾Kutupa kwa maso.
🌾Kutsekula mmimba.
🌾Chifuwa.
🌾 Chinfine.
🌾Kufooka kwa miyendo.
🌾Kunyentchera.
🌾Njoka za mmimba.
🌾 Kusowa kwa chilakolako chokudya (loss of Appetite).

👉 MK3,000 *Botolo laling'ono* (125grams).
👉 MK5,000 *Botolo lalikulu*( 250grams)

*Dosage*
▪️Sungunulani 3 teaspoons mmadzi a 1 litre.
🤏🏿3 days for prevention per week
🤏🏿5 days for treatment

*M'mawa*(MONDAY) pa *NANDOZ* from *8:00am* mpaka *2 koloko.*

Imbani📲 *0997286698 / 0889726008*

*Even Chicks recommend us🐣*

16/07/2022

*Likasa la Mlimi pa nkhani ya Feed Formulation*

●Muli ma Formula 65 ophweka kupanga, otchipa komanso ogwilitsa ntchito zipangizo za kwathu konkuno. Chicken's, Quails, Turkey's, Goat's, Sheep, Pigs, Cattle & Fish.
●A detailed information how to calculate the livestock feed formulas using the simple Pearson square method .
● Amazing secrets on usage of Cassava & sweet potato in livestock feed formulation.
● Let your feeds be medicine to your livestock. Feeds that doesn't only supply nutrients But also boosting immunity.
●Alternative to Premix, Potassium, Methionine, Lime & trace elements.
● Pig Concentrates. Easy to do & cheap. Do & sell to farmers around your area, it's all possible.
●Broiler & Layer Concentrates.

🚨So much more.

*Price : K15,000*

Tipezen ku area 25 along 49 - nsungwi road pa skeffa. *Hard copies ONLY.* We send elsewhere.

☎0982054911/0881941634.

*M-vetLivestockSolutions*

REMEMBER.We are still in the cold season so make sure that your birds are living in a very accommodative environment.In ...
07/07/2022

REMEMBER.

We are still in the cold season so make sure that your birds are living in a very accommodative environment.

In addition, Coccidiosis, Sneezing, Coughs and worms have advantage on the same.

Avoid wet or damaged bedding and low temperature (keep it warm)

Protect and treat Poultry diseases by using Magik Powder.

~Even Chicks recommend us~

*MAGIK POWDER* KU *BLANTYRE**KODI* ndinu Mlimi oweta Nkhuku, Zinziri, Nkhanga, Nkhunda, Nkhukutembo, Nkhwali, Njiwa koma...
31/05/2022

*MAGIK POWDER* KU *BLANTYRE*

*KODI* ndinu Mlimi oweta Nkhuku, Zinziri, Nkhanga, Nkhunda, Nkhukutembo, Nkhwali, Njiwa komanso Mbalame za mitundu yosiyanasiyana, *ndipo mukukumana ndi mavuto ngati 👇🏿awa*
📍Kutupa kwa maso ndi mitu
📍Chitosi cha magazi
📍Kugwetsa Mapiko
📍Chifuwa
📍Chimfine
📍Fowl Pox
📍Kufooka miyendo
📍Njoka za m'mimba
📍Kusowa kwa Chilakolako chokudya(Loss of Appetite)

*🌱 MK3,000* (125grams)
*🌱 MK5,000* (250grams)

*Mawa (WEDNESDAY)* pa *NANDOZ* from *8:00am* to *2 pm.*

Call *0997286698*/
*0889726008*

*A product of CFO Consults.*

*“Even Chicks recommend us "*

*MAGIK POWDER* KU *BLANTYRE**KODI* ndinu Mlimi oweta Nkhuku, Zinziri, Nkhanga, Nkhunda, Nkhukutembo, Nkhwali, Njiwa koma...
27/04/2022

*MAGIK POWDER* KU *BLANTYRE*

*KODI* ndinu Mlimi oweta Nkhuku, Zinziri, Nkhanga, Nkhunda, Nkhukutembo, Nkhwali, Njiwa komanso Mbalame za mitundu yosiyanasiyana, *ndipo mukukumana ndi mavuto ngati 👇🏿awa*
📍Kutupa kwa maso ndi mitu
📍Chitosi cha magazi
📍Kugwetsa Mapiko
📍Chifuwa
📍Chimfine
📍Fowl Pox
📍Kufooka miyendo
📍Njoka za m'mimba
📍Kusowa kwa Chilakolako chokudya(Loss of Appetite)

*🌱MK3,000* 125grams
*🌱MK5,000* 250grams

*Mawa (THURSDAY)* pa *NANDOZ* from *7:45am* to *2 pm.*

Call *0997286698*/
*0889726008*

*A product of CFO Consults.*

*“Even Chicks the recommend us "*

*MAGIK POWDER* KU *BLANTYRE*🕊️🦢🦃🐓🦆🦤🤏Mu *2022*, CHAKA CHA TSOPANO🤓.*MLIMI OTSOGOLA WAYAMBA KALE KUGWIKITSIRA NTCHITO* Mag...
17/01/2022

*MAGIK POWDER* KU *BLANTYRE*
🕊️🦢🦃🐓🦆🦤

🤏Mu *2022*, CHAKA CHA TSOPANO🤓.

*MLIMI OTSOGOLA WAYAMBA KALE KUGWIKITSIRA NTCHITO* Magik Powder.

Uwu ndi Mtera othana ndi Matenda ochuluka a Nkhuku ndi Mbalame ndi zinazonse:
🤏🏼Kutupa kwa Maso.
🤏🏼Chitosi cha magazi.
🤏🏼Chifuwa.
🤏🏼Chimfine.
🤏🏼Fowl Pox, Mycoplasma.
🤏🏼Kufooka miyendo.
🤏🏼Njoka za m'mimba.
🤏🏼Kusowa kwa Chilakolako chokudya(Loss 9f Appetite).

🌶️ Botolo laling'ono *MK2,000🤷‍♂️*

🌶️ Big bottle only at *MK4,000🤷‍♀️*

🤏🤓👇
TITHOKOZE AMENE MUKUMAIMBA MA FONI POTIUZA ZA MMENE MANKHWALA A MAGIC POWDER AKUTHANDIZIRANI.

CHONDE, MUWAUZEKO ANZANU ZA M'MENE MANKHWALAWA AKUKUTHANDIZIRANI KUTI ALIMI ANZANU APINDULE NAWO POGWIRISIRA NTCHITO MANKHWALAWA.

*M'mawa(Tuesday)* pa *NANDOZ* kuyambira *8:30* mpaka *2 koloko*

Imbani *0997286698*
*0889726008*

*A product of CFO Consults.*

*“Even Chicks recommend us 🐣"*

*Magik Powder KU BLANTYRE.*MULIMI APINDULENSO MU NYENGO ZA CHISANGALALO ZIKUBWERAZI*ALIMI OTSOGOLA, AMAGWILITSIRA NTCHIT...
30/11/2021

*Magik Powder KU BLANTYRE.*

MULIMI APINDULENSO MU NYENGO ZA CHISANGALALO ZIKUBWERAZI

*ALIMI OTSOGOLA, AMAGWILITSIRA NTCHITO Magik Powder.*

▪️Awa ndi mankhwala a *organic* (herbs) a mbalame monga nkhuku, zinziri, abakha, nkhunda, nkhanga ndi nkhukundembo.
▪️Mankhwalawa amathandiza ku matenda awa
🌾Chitosi cha magazi
🌾Kutupa kwa maso.
🌾Kutsekula mmimba.
🌾Chifuwa.
🌾 Chinfine.
🌾Kufooka kwa miyendo.
🌾Kunyentchera.
🌾Njoka za mmimba.
🌾 Kusowa kwa chilakolako chokudya (loss of Appetite).

👉 MK2,000 *Botolo laling'ono* (125grams).
👉 MK4,000 *Botolo lalikulu*( 250grams).

*Dosage*
▪️Sungunulani 3 teaspoons mmadzi a 1 litre.
🤏🏿3 days for prevention per week
🤏🏿5 days for treatment

🌶️TIBWEREZE KUNENA KUTI MAGIK POWDER, NDI MANKHWALA OSATI KATEMERA

*Bwerani Mmawa*(WEDNESDAY) pa *NANDOZ* from *8:00* malire *11 koloko.*

Imbani *0997286698 / 0889726008*

*A product of CFO Consults*

*Even the chicks🐣 recommend us*

*🐓2021 ORGANIC BROILER MANAGEMENT TRAINING🐓**LESSONS*🌴feed fermentation 🌴miracle combo🌴Herbal combo 🌴Biochar for litter ...
12/01/2021

*🐓2021 ORGANIC BROILER MANAGEMENT TRAINING🐓*

*LESSONS*
🌴feed fermentation
🌴miracle combo
🌴Herbal combo
🌴Biochar for litter and feeds
🌴multivitamin syrups and calcium
🌴Artificial insemination in Poultry
🌴LAB WITHOUT MILK
🌴Organic Bonus feeds for Kuroilers, broilers and Layers.
🌴Poultry Diseases and their organic treatment (All)
🌴Organic medication charts for broilers, Turkeys, Kuroilers and Layers
🌴Turkey Production
🌴Magic clove water

*And many more...*

JUST IMAGINE🤔;
👉 *Videos, PDFs (books), Charts, Audios and other tools, will be used where necessary🙂*

CHARGES: *MwK2,500 ONLY*

*Duration* ; 2 weeks intensive Online Training

TO REGISTER; *Call or Whatsapp:* 0992644460 / 0886811585

*Even chicks recommend us🐣*

06/10/2020

🐓CHICHEWA AND ENGLISH POULTRY TRAINING + 35 Free BOOKS (PDFs)🐓

*TWO WEEKS OF INTENSIVE ONLINE TRAINING IN POULTRY FARMING*

*Topics to be covered*
✅ Hatching strong and healthy chicks
✅ Tricks to ensure zero mortality
✅ Feed formulation (the Pearson square)
✅ How to Achieve maximum growth within a shortest time possible
✅ Housing and environment
✅ Vaccination, biosecurity and disease management (organic and inorganic way)
✅ Marketing your chickens.

*Bonus Topics:*

▪️ *Quail farming*
▪️ *Vaccination and feeding programs*

*Fees:* MK 1,000 ONLY🤷‍♂️
*Date:* 19th October, 2020.

*MUSANATUMUZE NDALAMA, FUNSANI:* 0997286698 *FOR MORE INFORMATION (THUS BEFORE SENDING MONEY).*
🐓🐓🐓🐓🐓🐓

TAMVANI *NKHANI YABWINO KWA NONSE AMENE MWALIPIRA KUTI MUTENGE NAWO MBALI MU MAPHUNZIRO OMWE AKUZAYAMBIDWA PA 19 OCTOBER, 2020.*

*MUKAZAMALIZA MAPHUNZIRO, MUZAPATSIDWA MABUKHU MWAULERE. TANGOGANIZANI, PAZAPEREKEDWA MABUKHU AWA:*

1). LOCAL CHICKEN FEED MALAWI (23 PAGES).
2). GUINEA FOWL (NKHANGA) FARMING IN MALAWI (50 PAGES).
3). PROFITABLE HENS REARING {POULTRY}(293 PAGES).
4). SASSO (CHICKENS) FARMERS GUIDE (8 PAGES).
5). IMPROVING THE PERFORMANCE OF LOCAL CHICKENS (30 PAGES).
6). QUAIL HOUSING (8 PAGES)
7). QUAIL PRODUCTION (32 PAGES).
8). MIKOLONGWE BLACK AUSTRALORP CHICKEN PRODUCTION (23 PAGES).
9). KIENYEJI CHICKEN PRODUCTION (34 PAGES).
10). KUROILER CHICKEN FARMING (80 PAGES).
11). INCUBATING AND HATCHING EGGS (13 PAGES).
12). COMMON INCUBATION PROBLEMS (6 PAGES).
13). DIFFERENT TYPES OF POULTRY HOUSING SYSTEM FOR TROPICAL CLIMATE (69 PAGES).
14). CHICKEN HOUSING STRUCTURES (14 PAGES).
15). BUSINESS PLAN TEMPLATE (22 PAGES).
16). HOW TO WRITE A BUSINESS PLAN (290 PAGES).
17). INVESTING FOR BEGINNERS {A COMPREHENSIVE BEGINNERS' GUIDE TO 18). SUCCESSFUL INVESTING (134 PAGES).
19). QUIT YOUR JOB FOLLOW YOUR PASSION AND BE RICH (77 PAGES).
20). FARM MANAGEMENT HANDBOOK (114 PAGES).
21). GUIDE TO AGRICULTURAL (CROP) PRODUCTION (365 PAGES).
22). SOIL FERTILITY MANAGEMENT (84 PAGES).
23). SWEET POTATO PRODUCTION (9 PAGES).
24). NON-CHEMICAL CROP PROTECTION (85 PAGES).
25). BANANA PLANTATION (65 PAGES).
26). CULTIVATION OF SOYA AND OTHER LEGUMES (70 PAGES).
27). CULTIVATION OF TOMATOES (93 PAGES).
28). HOW TO SUCCESSFULLY GROW IRISH POPTATOES (10 PAGES).
29). ONION'S GUIDELINES (5 PAGES).
30). A GUIDE FOR VEGETABLE GROWING (99 PAGES).
31). SMALL-SCALE MUSHROOM CULTIVATE (87 PAGES).
32). BEE KEEPING IN THE TROPICS (88 PAGES).
33). PIGGERY {PIG FARMING RESEARCH PROGRAM} (36 PAGES).
34). FARMER CROP AND LIVESTOCK RECORD BOOK (16 PAGES).
35). SAUSAGE RECIPES (106 PAGES)

ALL THESE 35 BOOKS, WILL BE GIVEN TO YOU AFTER THE TRAINING🐣.

SANKHANI MWANZERU🤔

*100% POULTRY FARMING TRAINING ➕ 30 PDFs (Free BOOKS)**ENA AMATIPEMPHA KUTI TIWALORE KULOWA MU MAPHUNZIRO A ZA NKHUKU NG...
26/09/2020

*100% POULTRY FARMING TRAINING ➕ 30 PDFs (Free BOOKS)*

*ENA AMATIPEMPHA KUTI TIWALORE KULOWA MU MAPHUNZIRO A ZA NKHUKU NGAKHALE INAYAMBA KALE( Pa 21st September, 2020),* LERO TIKUTI, *“TAKULANDIRANI"*

*SOME WERE ASKING FOR A FAVOR TO BE ALLOWED TO TAKE PART IN POULTRY TRAINING WHICH ALREADY STARTED ON 21st September, 2020,* TODAY *WE ARE ALLOWING YOU.*

THIS IS AN *ONLINE* poultry training ever, THAT STARTED on *21st SEPTEMBER, 2020*

*TOPICS:*

*UNIT 1. GETTING STARTED*
✍️ Finding a perfect niche for you within poultry farming
✍️ What you need as a farmer to succeed
✍️ Designing your chicken house
✍️ Breed selection, breeding and brooding your chicks.
✍️ Chicken health and vaccination
✍️ Record keeping
*UNIT 2. MAKE YOUR OWN FEED*
*==================*
✍️ Introduction to feed making
✍️ Getting to know feed formulation techniques
✍️ The Pearson square method
✍️ The Graph method
✍️ The Substitution method
✍️ Trial and error method
✍️ The computer software method
*==================*
*UNIT 3. CHICKEN DISEASE - PREVENTION AND CONTROL*
✍️ Health and disease management
✍️Disease prevention
✍️ Disease treatment
✍️ Important chicken diseases
✍️ Medication and vaccination
*==================*
*UNIT 4. SELL LIKE A BOSS*
✍️ Marketing your chickens
✍️ Marketing strategies
✍️ Value creation
✍️ Creating a competitive advantage
✍️ Challenging a competitive advantage
*==================*
*REMEMBER,* THIS IS A WHATSAPP TRAINING.
*Duration:* 3 weeks.

*NOTE:* TRAINING IS IN PROGRESS SINCE 21st September, 2020.

*Fee:* K1,000 Only *for the whole Training.*

WHATSAPP: *+265 997 286 698* TO BE ADDED.

*NKHANI YABWINO KWA ONSE AMENE MWALIPIRA KUTI MUTENGE NAWO MBALI MU MAPHUNZIRO AMENEWA🐓*

*MUKAZAMALIZA MAPHUNZIRO, MUZAPATSIDWA MABUKHU MWAULERE.*

*TANGOGANIZANI, PAZAPEREKEDWA MABUKHU AWA:*

1). ORGANIC POULTRY PRODUCTION (99 PAGES).
2). BROILER PRODUCTION including feeding (12 PAGES).
3). GUIDELINES FOR BROILER FEEDING(32 PAGES).
4). CHICK BROODING (2 PAGES).

AMONG OTHER BOOKS

WE PRESENT,*TG DYNAMIC INVESTMENTS*WITH:                     *🐓ORGANICALLY REARED BROILER CHICKENS.🐓*                   ...
17/08/2020

WE PRESENT,
*TG DYNAMIC INVESTMENTS*

WITH:

*🐓ORGANICALLY REARED BROILER CHICKENS.🐓*
REMEMBER;
1). WE DO NOT GIVE BOOSTER CHEMICAL TREATMENT TO OUR CHICKENS.
2). WE USUALLY SELL THEM AT 7TH WEEK, MEANING THAT, WE SELL THEM WELL MATURED.
3). WE DELIVER EVERYWHERE.

PRICES:
*MK 2,800 PER ONE CHICKEN.*
*MK 2,700 PER CHICKEN IF YOU BUY 30 CHICKENS AND ABOVE.*
WE ARE STILL RESIDING IN BLANTYRE AT MANDALA.

*FOR MORE INFORMATION, CALL/THE WHATSAPP; The C.E.O: +265 888 99 40 40 The Marketing Director, Michael MP Mataka: +265 997 28 66 98.*

HURRY TO BOOK AND BUY, BECAUSE WE HAVE JUST OPENED AND PEOPLE ARE COMING IN LARGE NUMBERS.

*TG DYNAMIC INVESTMENTS,* WE ARE THE BEST!!!
🐓🐓🐓🐓🐓🐓

Address

Machinga
Machinga

Telephone

+265888994040

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when T.G. Dynamic Investments in All Poultry Businesses - Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to T.G. Dynamic Investments in All Poultry Businesses - Malawi:

Share