SMAM

SMAM Musatitengele ife kokatiyesa, kma mutipulumuse ife kwa oyipayo πŸ™πŸΏπŸ˜Ž

get you Stingy Men ID here βœ” https://smam-official.netlify.app/ #/id-generator

πŸ‘€πŸ€¦πŸΏβ€β™‚οΈ apatu sizinayende boys
14/05/2026

πŸ‘€πŸ€¦πŸΏβ€β™‚οΈ apatu sizinayende boys

09/05/2026

Ifeso ngat SMAM tili mbali ya bamboyo 😭🀣

25/04/2026

Anthu mwakololatu πŸ™„ mupange nzinkhoswe muthe chimanga πŸ€¦πŸΎβ€β™‚οΈπŸ€£

21/04/2026

anabwelatu ndimoto πŸ€£πŸ€¦β€β™€οΈ ma chairman kumusekelela

nde ndizitu. Oyipa nd oyipa basi

15/04/2026

Kodi mesa timalesa kukonda akazi, 🀣😭

-official

14/04/2026

potengela mgwilizano omwe akuluakulu a SMAM anapanga zulo.....

tagwilizana zot a Shipmark alandidwe ID yawo chifukwa cha zoyankhula zawo zobwelesa chisokonezo ku SMAM. 😭 A Shipmark amalimbikisa ma chairman kt tiziononga chuma chathu pongogawa mopusa zomwe malamulo a SMAM amalesa [FIRST STINGY AMENDMENT βœ”βš–]. Bungweli lati lithana ndi aliyense ofuna kusokoneza ma chairman athu.
~~~~~~~~~~~~~
Follow for more updates and laughter🀣

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SMAM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category